VERSE 1
Titavaya koyezetsa nkundipeza nako ndekhaaaa
Ntakhala osabereka ungakhalebe
Dekhaaaaa?

Ukandipepha dola masaka nkukupatsa
Nditakhala ndimakaba ungakhalebe ofatsa?

Ndimagona kwathu iwe umagona kwanu
Stern yanga itakuuza
Abatiya amabwebweta

Iweyo ungalimbe kapena uthaaaaa kufoka
Nditakha bawa ai koma fodya ndimakoka

Umadziwa Fanz imakadya mahule
Nditakha ndimava usiku uliwonse

Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani
Ndikufuna ndingodziwa chonde
Undimasukire

CHORUS /HOOK

Undimasukire babieeeee
Ndikufuna ndidziweeee yeeeh yeeeh

Ndati pali zinthu zina zomwe sumadziwa mami
Zokhudza ine zokhudza iweso

Nanga nditakhala chonchi ungata?
Nanga zitakhala chonchi ungata?

Iweyo
Ndikufuna ndidziweeeee
Zitakhalaaaa chonchiii

VERSE 2
Nditakhala sinkufuna koma iwe osamaona
Ndimaganiza zaiwe pokha pokha nkakuona

Kuti ndimalowa tchetchi kufuna
Kunamizaa
Pogonaso ndimakodza tulo sungalipeza

Zitakha ndimakukonda cha zomwe ulinazo
Kuti zosezi zitatha chikondi chidzatha

Kwanu kumasowa nkhuku, nditakhala ndine
Kuti zovala izizi sizaine zama friends

Ndimadziwa umanyada kwa anzakoooo zaa ine
Nditakhala ndimatamba usiku mawuruka
Kodi zitakhala chonchi iweyo ungatani
Ndikufuna ndingodziwa chonde
Undimasukire

BACK TO CHORUS/HOOK

BRIDGE
Nanga zitakhala chonchi ungata?
Iweyo
(Ndikufuna ndidziwe)
Nanga zitakhala chonchi ungataaaaaaaaa?

Ndikuna ndidziwe
Ngati uli wa ineyoooo Babie yeahhhhhh
Ndimasukile

Ndikufuna ndidziweeeeeeeeeeeee

BACK TO CHORUS/HOOK (X2)
Correct  |  Mail  |  Print  |  Vote

Zitakhala Chonchi Lyrics

Abatiya – Zitakhala Chonchi Lyrics

More Abatiya lyrics