[Intro]

Abatiya on this one

Oh oh oh oh
Ahhh
Nah nah nah
Eeeeeye

[Chorus]

NdiKusowa kwanga .
Pamasowa pake
(aku sa nduka
Chitonzo)

Anawaaaa
Alera bwanji
Opanda bambo awo pafupi

Akasowa chakudya
(Mupatse nkono)

Akasowa chovala
(Mupatse nkono)

Akasowa pokhala
(Mupatse nkono oooooooooh)

Mmmmh

[Verse 1]

Zimathekaa akasowa nchere
Amangogwetsa misonzi

AkakumbukaaAaaa
Moyo wake unali ophwekaaa

Zoti angamapephe
Iyeyu

Sankayembekezera

Koma kuchoka kwanga padziko
Kunasitha nyengoo zakeee

[Chorus X 2]

NdiKusowa kwanga .
Pamasowa pake
(aku sa nduka
Chitonzo)

Anawaaaa
Alera bwanji
Opanda bambo awo pafupi

Akasowa chakudya
(Mupatse nkono)

Akasowa chovala
(Mupatse nkono)

Akasowa pokhala
(Mupatse nkono oooooooooh)

Mmmmh

[Verse 2]

Amayesa ma bizinez
(Mapeto ake amaduka)

Nzeru nzake zinatha uyu
Amalakalaka ndili moyo

Anawonse apulukira
(Wankulu uja ndi Mbava)

Ang'ono ang'o samuveraaaaa
Sukulu anasiya kale kale

[Chorus X 2]

[Bridge]

Mupatse nkono
Mupatse nkono
Mupatse nkono

Eh
Correct  |  Mail  |  Print  |  Vote

Mupatse Nkono Lyrics

Abatiya – Mupatse Nkono Lyrics

More Abatiya lyrics