VERSE TWO
Yako fandum
Ngat yochita kupanga zoom
Ndikondwa mudzi wako onseu ndine mfumu
Unamatamatako konse sunasiye room
Ena kumayesera kuti alowe koma hmmm?
Ndimakondwera ndikamaona ka view.
Nde iweyo ameneyo everyday u look brand new
Ndichikondi chako chomwe chindipatsa mphamvu
Zonsezi in one sentence honey I love you
Kukusiya iwe ndikuluza timing
Poti munyengo yaziphaliwali u stood by me
In so doing unawina chikondi cha ine
Mpaka muyaya ndiri nawe n'patse poti nsaine.
Unakhulupira mwa ine kuchoka pa chyambi
Ndisanapsetsetse ndikumveka khambi.
Pano ndapsano umveno ku-kukoma kwa changachi
Chikondi
Udzingopanga download.
VERSE THREE
Mu mvula ya ziphaliwaliwali unandikonda more
Kumangofeela warm – kumangofeela bho
Kuthamangitsa zinthu zanga zikamayenda slow
Kumangofeela bho – kumangofeela bho
Si inenso wamanyazi sweetie you make me stand tall
Kumangofeela bho – ine kumangofeela bho
Usiku usanagone kundimenyera ka call
Kumangofeela bho – kumangofeela bho