top 100
·
top new
·
updates
·
submit lyrics
#
A
B
C
D
E
F
G
H
I
J
K
L
M
N
O
P
Q
R
S
T
U
V
W
X
Y
Z
Correct Malawi Native Anthem Text Lyrics
Lyrics
►
Artists: N
►
National Anthem
►
Correct Malawi Native Anthem Text
Artist:
Song:
Comment:
Lyrics:
1. Mlungu dalitsani Malawi, Mumsunge m'mtendere. Gonjetsani adani onse, Njala, nthenda, nsanje. Lunzitsani mitima yathu, Kuti tisaope. Mdalitse Mtsogo leri na fe, Ndi Mai Malawi. 2. Malawi ndziko lokongola, La chonde ndi ufulu, Nyanja ndi mphepo ya m'mapiri, Ndithudi tadala. Zigwa, mapiri, nthaka, dzinthu, N'mphatso zaulere. Nkhalango, madambo abwino. Ngwokoma Malawi. 3. O! Ufulu tigwirizane, Kukweza Malawi. Ndi chikondi, khama, kumvera, Timutumikire. Pa nkhondo nkana pa mtendere, Cholinga n'chimodzi. Mai, bambo, tidzipereke, Pokweza Malawi. Sent by Carlos André Pereira da Silva Branco
add rows