Innocent P. Makuwira - Kwathu Sipadziko lyrics | LyricsFreak
Correct  |  Mail  |  Print  |  Vote

Kwathu Sipadziko Lyrics

Innocent P. Makuwira – Kwathu Sipadziko Lyrics

Kwathu sipadziko ndingopitilira;
Ndazikundikira chuma kumwambako
Mngelo akodola pakhomo lammwamba
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
Mbuye ndinu bwenzi langa ndithu
Ndichitenji ngati kumwambako sikwathu
Mngelo akodola pakhomo lammwamba
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu.
Mayi watsogola muulemelero
Ndifuna kugwira dzanja lake, konko
Andiyembekeza chinthuchi ndidziwa
Ndipo dziko lapansi sindiyesa kwathu
Share lyrics
×

Kwathu Sipadziko comments